2 Samueli 21:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kenako anthu anaika mafupa a Sauli ndi a mwana wake Yonatani mʼdera la Benjamini ku Zela+ mʼmanda a Kisi+ bambo ake. Atachita zonse zimene mfumu inalamula, Mulungu anamvetsera madandaulo awo okhudza dzikolo.+
14 Kenako anthu anaika mafupa a Sauli ndi a mwana wake Yonatani mʼdera la Benjamini ku Zela+ mʼmanda a Kisi+ bambo ake. Atachita zonse zimene mfumu inalamula, Mulungu anamvetsera madandaulo awo okhudza dzikolo.+