2 Samueli 21:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiyeno panayambikanso nkhondo pakati pa Afilisiti ndi Aisiraeli.+ Choncho Davide ndi atumiki ake anapita kukamenyana ndi Afilisiti, koma Davide anatopa kwambiri. 2 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:15 Nsanja ya Olonda,1/15/2013, ptsa. 30-31
15 Ndiyeno panayambikanso nkhondo pakati pa Afilisiti ndi Aisiraeli.+ Choncho Davide ndi atumiki ake anapita kukamenyana ndi Afilisiti, koma Davide anatopa kwambiri.