2 Samueli 21:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Nkhondo imeneyi itatha, panayambikanso nkhondo ina yomenyana ndi Afilisiti+ ku Gobu. Pa nthawi imeneyo Sibekai+ wa ku Husa* anapha Safi, mbadwa ya Arefai.+
18 Nkhondo imeneyi itatha, panayambikanso nkhondo ina yomenyana ndi Afilisiti+ ku Gobu. Pa nthawi imeneyo Sibekai+ wa ku Husa* anapha Safi, mbadwa ya Arefai.+