2 Samueli 21:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kenako panayambikanso nkhondo ina ndi Afilisiti+ ku Gobu, ndipo Elihanani mwana wa Yaare-oregimu wa ku Betelehemu anapha Goliyati wa ku Gati, amene mtengo wa mkondo wake unali waukulu ngati mtengo wogwiritsa ntchito powomba nsalu.+
19 Kenako panayambikanso nkhondo ina ndi Afilisiti+ ku Gobu, ndipo Elihanani mwana wa Yaare-oregimu wa ku Betelehemu anapha Goliyati wa ku Gati, amene mtengo wa mkondo wake unali waukulu ngati mtengo wogwiritsa ntchito powomba nsalu.+