2 Samueli 21:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kenako panayambikanso nkhondo ina ku Gati ndipo kunali munthu wamkulu modabwitsa. Iye anali ndi zala 6 kudzanja lililonse ndiponso zala 6 kuphazi lililonse, moti anali ndi zala 24. Nayenso anali mbadwa ya Arefai.+
20 Kenako panayambikanso nkhondo ina ku Gati ndipo kunali munthu wamkulu modabwitsa. Iye anali ndi zala 6 kudzanja lililonse ndiponso zala 6 kuphazi lililonse, moti anali ndi zala 24. Nayenso anali mbadwa ya Arefai.+