2 Samueli 21:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Iye ankanyoza kwambiri Aisiraeli.+ Choncho Yonatani mwana wa Simeyi,+ mchimwene wake wa Davide, anamupha. 2 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:21 Nsanja ya Olonda,1/1/1989, tsa. 28
21 Iye ankanyoza kwambiri Aisiraeli.+ Choncho Yonatani mwana wa Simeyi,+ mchimwene wake wa Davide, anamupha.