2 Samueli 22:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pansi pa nyanja panaonekera;+Maziko a dziko lapansi anaonekera chifukwa cha kudzudzula kwa Yehova,Chifukwa cha mphamvu ya mpweya wotuluka mʼmphuno mwake.+
16 Pansi pa nyanja panaonekera;+Maziko a dziko lapansi anaonekera chifukwa cha kudzudzula kwa Yehova,Chifukwa cha mphamvu ya mpweya wotuluka mʼmphuno mwake.+