2 Samueli 22:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndidzakhalabe wosalakwa+ pamaso pake,Ndipo ndidzayesetsa kupewa cholakwa.+