2 Samueli 23:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Awa ndi mawu omaliza a Davide:+ “Mawu a Davide mwana wa Jese,+Mawu a munthu amene anakwezedwa mʼmwamba,+Wodzozedwa+ wa Mulungu wa Yakobo,Munthu woimba bwino nyimbo+ za Isiraeli.
23 Awa ndi mawu omaliza a Davide:+ “Mawu a Davide mwana wa Jese,+Mawu a munthu amene anakwezedwa mʼmwamba,+Wodzozedwa+ wa Mulungu wa Yakobo,Munthu woimba bwino nyimbo+ za Isiraeli.