2 Samueli 23:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma anthu onse opanda pake amawakankhira kutali+ ngati zitsamba zaminga,Chifukwa zitsamba zamingazo sangazinyamule ndi manja pozichotsa.
6 Koma anthu onse opanda pake amawakankhira kutali+ ngati zitsamba zaminga,Chifukwa zitsamba zamingazo sangazinyamule ndi manja pozichotsa.