-
2 Samueli 23:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Munthu akamazigwira,
Ayenera kukhala ndi zipangizo zachitsulo komanso mtengo wa mkondo,
Ndipo ziyenera kutenthedwa ndi moto nʼkupseratu pamene zinamera.”
-