2 Samueli 23:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Awa ndi mayina a asilikali amphamvu a Davide:+ Yosebu-basebete mbadwa ya Hakemoni, mtsogoleri wa amuna atatu.+ Iye anatenga mkondo wake nʼkupha anthu 800 nthawi imodzi. 2 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 23:8 Nsanja ya Olonda,10/1/2005, tsa. 10
8 Awa ndi mayina a asilikali amphamvu a Davide:+ Yosebu-basebete mbadwa ya Hakemoni, mtsogoleri wa amuna atatu.+ Iye anatenga mkondo wake nʼkupha anthu 800 nthawi imodzi.