2 Samueli 23:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Womutsatira anali Eliezara+ mwana wa Dodo+ mwana wa Ahohi. Iye anali mmodzi mwa asilikali atatu amphamvu amene anali ndi Davide pamene ankanyoza Afilisiti. Iwo anasonkhana kumeneko kuti amenye nkhondo. Ndipo amuna a Isiraeli atathawa,
9 Womutsatira anali Eliezara+ mwana wa Dodo+ mwana wa Ahohi. Iye anali mmodzi mwa asilikali atatu amphamvu amene anali ndi Davide pamene ankanyoza Afilisiti. Iwo anasonkhana kumeneko kuti amenye nkhondo. Ndipo amuna a Isiraeli atathawa,