2 Samueli 23:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Eliezara sanathawe ndipo anapitiriza kupha Afilisiti mpaka dzanja lake linatopa nʼkuchita dzanzi.+ Moti tsiku limenelo Yehova anawathandiza kuti apambane+ ndipo anthu ena onse ankabwera mʼmbuyo mwake nʼkumatenga zinthu za anthu ophedwawo.
10 Eliezara sanathawe ndipo anapitiriza kupha Afilisiti mpaka dzanja lake linatopa nʼkuchita dzanzi.+ Moti tsiku limenelo Yehova anawathandiza kuti apambane+ ndipo anthu ena onse ankabwera mʼmbuyo mwake nʼkumatenga zinthu za anthu ophedwawo.