2 Samueli 23:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Atsogoleri atatu mwa atsogoleri 30 anapita kwa Davide kuphanga la Adulamu+ pa nthawi yokolola. Apa nʼkuti Afilisiti atamanga matenti mʼchigwa cha Arefai.+
13 Atsogoleri atatu mwa atsogoleri 30 anapita kwa Davide kuphanga la Adulamu+ pa nthawi yokolola. Apa nʼkuti Afilisiti atamanga matenti mʼchigwa cha Arefai.+