2 Samueli 23:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pa nthawiyi nʼkuti Davide ali kumalo ovuta kufikako,+ ndipo mudzi wa asilikali a Afilisiti unali ku Betelehemu.
14 Pa nthawiyi nʼkuti Davide ali kumalo ovuta kufikako,+ ndipo mudzi wa asilikali a Afilisiti unali ku Betelehemu.