2 Samueli 23:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Iye anati: “Sindingachite zimenezi inu Yehova! Kodi ndimwe magazi+ a amuna amene anaika moyo wawo pangozi kuti akatunge madziwa?” Choncho iye anakana kumwa madziwo. Izi nʼzimene asilikali atatu amphamvuwo anachita. 2 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 23:17 Mulungu Azikukondani, tsa. 91 ‘Mulungu Apitirize Kukukondani’, ptsa. 76-77 Nsanja ya Olonda,5/15/2005, tsa. 19
17 Iye anati: “Sindingachite zimenezi inu Yehova! Kodi ndimwe magazi+ a amuna amene anaika moyo wawo pangozi kuti akatunge madziwa?” Choncho iye anakana kumwa madziwo. Izi nʼzimene asilikali atatu amphamvuwo anachita.
23:17 Mulungu Azikukondani, tsa. 91 ‘Mulungu Apitirize Kukukondani’, ptsa. 76-77 Nsanja ya Olonda,5/15/2005, tsa. 19