2 Samueli 23:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Abisai,+ mchimwene wake wa Yowabu mwana wa Zeruya+ anali mtsogoleri wa anthu ena atatu. Iye anatenga mkondo wake nʼkupha anthu 300. Abisai anali wotchuka ngati amuna atatu aja.+
18 Abisai,+ mchimwene wake wa Yowabu mwana wa Zeruya+ anali mtsogoleri wa anthu ena atatu. Iye anatenga mkondo wake nʼkupha anthu 300. Abisai anali wotchuka ngati amuna atatu aja.+