-
2 Samueli 23:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Ngakhale kuti anali wolemekezeka kwambiri kuposa amuna 30 aja, sankafanana ndi amuna atatu aja. Koma Davide anamuika kukhala mmodzi wa asilikali ake omulondera.
-