2 Samueli 23:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Asaheli+ mchimwene wake wa Yowabu anali mʼgulu la amuna 30 aja. Mʼgululi munalinso Elihanani mwana wa Dodo wa ku Betelehemu,+
24 Asaheli+ mchimwene wake wa Yowabu anali mʼgulu la amuna 30 aja. Mʼgululi munalinso Elihanani mwana wa Dodo wa ku Betelehemu,+