2 Samueli 24:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Yehova anakwiyiranso kwambiri Aisiraeli+ pamene winawake anaukira Aisiraeli nʼkuuza Davide kuti: “Pitani mukawerenge+ anthu a Isiraeli ndi Yuda.”+ 2 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 24:1 Nsanja ya Olonda,5/15/2005, tsa. 197/15/1992, tsa. 5
24 Yehova anakwiyiranso kwambiri Aisiraeli+ pamene winawake anaukira Aisiraeli nʼkuuza Davide kuti: “Pitani mukawerenge+ anthu a Isiraeli ndi Yuda.”+