2 Samueli 24:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Choncho mfumu inauza Yowabu+ mkulu wa magulu ankhondo amene anali naye kuti: “Upite mʼmafuko onse a Isiraeli kuyambira ku Dani mpaka ku Beere-seba+ ndipo ukawerenge anthu kuti ndidziwe chiwerengero chawo.”
2 Choncho mfumu inauza Yowabu+ mkulu wa magulu ankhondo amene anali naye kuti: “Upite mʼmafuko onse a Isiraeli kuyambira ku Dani mpaka ku Beere-seba+ ndipo ukawerenge anthu kuti ndidziwe chiwerengero chawo.”