-
2 Samueli 24:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Koma Yowabu anauza mfumu kuti: “Yehova Mulungu wanu awonjezere anthu kuwirikiza ka 100 ndipo inu mbuyanga mfumu muone zimenezi zikuchitika. Koma nʼchifukwa chiyani mukufuna kuchita zimenezi mbuyanga mfumu?”
-