2 Samueli 24:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma mfumu inakana kumvera zimene Yowabu ndi atsogoleri a asilikali ananena. Choncho Yowabu ndi atsogoleri a asilikaliwo anapita kukawerenga Aisiraeli.+
4 Koma mfumu inakana kumvera zimene Yowabu ndi atsogoleri a asilikali ananena. Choncho Yowabu ndi atsogoleri a asilikaliwo anapita kukawerenga Aisiraeli.+