2 Samueli 24:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Atachoka kumeneko anafika mumzinda wa mpanda wolimba wa Turo+ ndiponso mʼmizinda yonse ya Ahivi+ ndi Akanani.+ Kenako anafika ku Beere-seba+ ku Negebu, mʼdziko la Yuda.
7 Atachoka kumeneko anafika mumzinda wa mpanda wolimba wa Turo+ ndiponso mʼmizinda yonse ya Ahivi+ ndi Akanani.+ Kenako anafika ku Beere-seba+ ku Negebu, mʼdziko la Yuda.