2 Samueli 24:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yowabu anapereka kwa mfumu chiwerengero cha anthu onse. Aisiraeli anali ndi asilikali 800,000 amphamvu okhala ndi lupanga, ndipo Ayuda anali ndi asilikali 500,000.+ 2 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 24:9 Nsanja ya Olonda,7/15/1992, tsa. 5
9 Yowabu anapereka kwa mfumu chiwerengero cha anthu onse. Aisiraeli anali ndi asilikali 800,000 amphamvu okhala ndi lupanga, ndipo Ayuda anali ndi asilikali 500,000.+