2 Samueli 24:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma Davide atawerenga anthuwo, anayamba kuvutika mumtima mwake.*+ Choncho Davide anauza Yehova kuti: “Ndachimwa+ kwambiri pochita zimenezi. Chonde Yehova, ndikhululukireni tchimo langa ine mtumiki wanu,+ chifukwa ndachita zopusa kwambiri.”+
10 Koma Davide atawerenga anthuwo, anayamba kuvutika mumtima mwake.*+ Choncho Davide anauza Yehova kuti: “Ndachimwa+ kwambiri pochita zimenezi. Chonde Yehova, ndikhululukireni tchimo langa ine mtumiki wanu,+ chifukwa ndachita zopusa kwambiri.”+