2 Samueli 24:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho Gadi anapita kwa Davide nʼkumuuza kuti: “Kodi mʼdziko lanu mugwe njala zaka 7?+ Kapena muzithawa adani anu kwa miyezi itatu?+ Kapena mʼdziko lanu mugwe mliri masiku atatu?+ Ganizirani mofatsa zoti ndikayankhe kwa amene wandituma.”
13 Choncho Gadi anapita kwa Davide nʼkumuuza kuti: “Kodi mʼdziko lanu mugwe njala zaka 7?+ Kapena muzithawa adani anu kwa miyezi itatu?+ Kapena mʼdziko lanu mugwe mliri masiku atatu?+ Ganizirani mofatsa zoti ndikayankhe kwa amene wandituma.”