2 Samueli 24:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Davide atamva zimenezo, anauza Gadi kuti: “Zimenezi zikundisowetsa mtendere kwambiri. Kuli bwino ndilangidwe ndi Yehova,+ chifukwa chifundo chake nʼchachikulu,+ koma ndisalangidwe ndi munthu.”+
14 Davide atamva zimenezo, anauza Gadi kuti: “Zimenezi zikundisowetsa mtendere kwambiri. Kuli bwino ndilangidwe ndi Yehova,+ chifukwa chifundo chake nʼchachikulu,+ koma ndisalangidwe ndi munthu.”+