2 Samueli 24:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kenako Yehova anagwetsa mliri+ mu Isiraeli kuyambira mʼmawa mpaka nthawi yomwe anakonza, moti anthu 70,000 anafa,+ kuyambira ku Dani mpaka ku Beere-seba.+
15 Kenako Yehova anagwetsa mliri+ mu Isiraeli kuyambira mʼmawa mpaka nthawi yomwe anakonza, moti anthu 70,000 anafa,+ kuyambira ku Dani mpaka ku Beere-seba.+