2 Samueli 24:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Davide ataona mngelo amene ankapha anthuyo anauza Yehova kuti: “Ine ndi amene ndachimwa, ndipo ine ndi amene ndalakwitsa, nanga nkhosazi+ zalakwa chiyani? Bwanji mulange ineyo ndi anthu amʼnyumba ya bambo anga?”+ 2 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 24:17 Nsanja ya Olonda,5/15/2005, tsa. 19
17 Davide ataona mngelo amene ankapha anthuyo anauza Yehova kuti: “Ine ndi amene ndachimwa, ndipo ine ndi amene ndalakwitsa, nanga nkhosazi+ zalakwa chiyani? Bwanji mulange ineyo ndi anthu amʼnyumba ya bambo anga?”+