2 Samueli 24:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kenako Gadi anapita kwa Davide tsiku lomwelo nʼkukamuuza kuti: “Pitani mukamangire Yehova guwa lansembe pamalo opunthira mbewu a Arauna wa Chiyebusi.”+
18 Kenako Gadi anapita kwa Davide tsiku lomwelo nʼkukamuuza kuti: “Pitani mukamangire Yehova guwa lansembe pamalo opunthira mbewu a Arauna wa Chiyebusi.”+