-
2 Samueli 24:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Arauna atasuzumira panja anaona mfumu ndi atumiki ake akubwera. Nthawi yomweyo Arauna anatuluka nʼkugwada pamaso pa mfumu ndipo anawerama mpaka nkhope yake kufika pansi.
-