24 Koma mfumu inauza Arauna kuti: “Ayi, ndikuyenera kugula zimenezi. Sindingapereke nsembe zopsereza kwa Yehova Mulungu wanga popanda kulipira chilichonse.” Choncho Davide anagula malo opunthira mbewu ndi ngʼombe ndipo analipira ndalama zokwana masekeli 50 asiliva.+