2 Samueli 24:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Zitatero, Davide anamangira Yehova guwa lansembe+ pamalowo ndipo anapereka nsembe zopsereza ndi nsembe zamgwirizano. Choncho Yehova anamva kuchonderera kwawo,+ moti mliri umene unagwa mu Isiraeliwo, unatha.
25 Zitatero, Davide anamangira Yehova guwa lansembe+ pamalowo ndipo anapereka nsembe zopsereza ndi nsembe zamgwirizano. Choncho Yehova anamva kuchonderera kwawo,+ moti mliri umene unagwa mu Isiraeliwo, unatha.