1 Mafumu 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Mfumu Davide anakalamba+ ndipo anali ndi zaka zambiri. Ankamufunditsa zofunda koma sankamva kutentha.
1 Mfumu Davide anakalamba+ ndipo anali ndi zaka zambiri. Ankamufunditsa zofunda koma sankamva kutentha.