1 Mafumu 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pa nthawi imeneyi Adoniya+ mwana wa Hagiti anayamba kudzikweza nʼkumanena kuti: “Ineyo ndikhala mfumu!” Iye anapangitsa galeta ndipo anali ndi amuna okwera pamahatchi* komanso amuna 50 oti azithamanga patsogolo pake.+ 1 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:5 Nsanja ya Olonda,7/1/2005, ptsa. 28-29
5 Pa nthawi imeneyi Adoniya+ mwana wa Hagiti anayamba kudzikweza nʼkumanena kuti: “Ineyo ndikhala mfumu!” Iye anapangitsa galeta ndipo anali ndi amuna okwera pamahatchi* komanso amuna 50 oti azithamanga patsogolo pake.+