1 Mafumu 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kenako Natani+ anauza Bati-seba+ mayi ake a Solomo+ kuti: “Kodi mwamva zoti Adoniya,+ mwana wa Hagiti, wakhala mfumu koma mbuye wathu Davide sakudziwa chilichonse?
11 Kenako Natani+ anauza Bati-seba+ mayi ake a Solomo+ kuti: “Kodi mwamva zoti Adoniya,+ mwana wa Hagiti, wakhala mfumu koma mbuye wathu Davide sakudziwa chilichonse?