-
1 Mafumu 1:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Bati-seba anagwada nʼkuweramira mfumu ndipo mfumuyo inati: “Ukufuna kupempha chiyani?”