1 Mafumu 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Iye wapereka nsembe zambiri za ngʼombe zamphongo, nyama zonenepa ndiponso nkhosa. Komanso waitana ana onse a mfumu, wansembe Abiyatara ndi Yowabu mkulu wa asilikali,+ koma mtumiki wanu Solomo sanamuitane.+
19 Iye wapereka nsembe zambiri za ngʼombe zamphongo, nyama zonenepa ndiponso nkhosa. Komanso waitana ana onse a mfumu, wansembe Abiyatara ndi Yowabu mkulu wa asilikali,+ koma mtumiki wanu Solomo sanamuitane.+