-
1 Mafumu 1:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Mukapanda kutero, inuyo mbuyanga mfumu mukadzangogona mʼmanda mofanana ndi makolo anu, ineyo ndi mwana wanga Solomo tidzaonedwa ngati oukira.”
-