1 Mafumu 1:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Mfumuyo inawauza kuti: “Tengani atumiki a mbuye wanu nʼkukweza Solomo mwana wanga panyulu* yanga,+ ndipo mupite naye ku Gihoni.+
33 Mfumuyo inawauza kuti: “Tengani atumiki a mbuye wanu nʼkukweza Solomo mwana wanga panyulu* yanga,+ ndipo mupite naye ku Gihoni.+