1 Mafumu 1:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Kumeneko, wansembe Zadoki ndi mneneri Natani akamudzoze+ kukhala mfumu ya Isiraeli. Ndiyeno mukalize lipenga nʼkunena kuti, ‘Mfumu Solomo akhale ndi moyo wautali!’+
34 Kumeneko, wansembe Zadoki ndi mneneri Natani akamudzoze+ kukhala mfumu ya Isiraeli. Ndiyeno mukalize lipenga nʼkunena kuti, ‘Mfumu Solomo akhale ndi moyo wautali!’+