1 Mafumu 1:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Mmene Yehova anakhalira ndi inu mbuyanga mfumu, akhalenso ndi Solomo+ ndipo achititse mpando wake wachifumu kukhala waukulu kuposa mpando wanu wachifumu, mbuyanga Mfumu Davide.”+
37 Mmene Yehova anakhalira ndi inu mbuyanga mfumu, akhalenso ndi Solomo+ ndipo achititse mpando wake wachifumu kukhala waukulu kuposa mpando wanu wachifumu, mbuyanga Mfumu Davide.”+