1 Mafumu 1:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Kenako wansembe Zadoki, mneneri Natani, Benaya+ mwana wa Yehoyada, Akereti ndi Apeleti+ anapita kukakweza Solomo panyulu ya Mfumu Davide+ nʼkupita naye ku Gihoni.+
38 Kenako wansembe Zadoki, mneneri Natani, Benaya+ mwana wa Yehoyada, Akereti ndi Apeleti+ anapita kukakweza Solomo panyulu ya Mfumu Davide+ nʼkupita naye ku Gihoni.+