1 Mafumu 1:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Atatero anthuwo anayamba kumulondola ndipo ankaimba zitoliro akusangalala kwambiri, moti nthaka inangʼambika chifukwa cha phokoso lawo.+
40 Atatero anthuwo anayamba kumulondola ndipo ankaimba zitoliro akusangalala kwambiri, moti nthaka inangʼambika chifukwa cha phokoso lawo.+