-
1 Mafumu 1:45Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
45 Kenako wansembe Zadoki ndi mneneri Natani anakamudzoza ufumu ku Gihoni. Ndiyeno abwerako akusangalala ndipo mumzinda muli phokoso lokhalokha. Phokoso limenelo ndi limene munamva lija.
-