-
1 Mafumu 1:47Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
47 Kuwonjezera apo, atumiki a mfumu abwera kudzafunira mafuno abwino mbuye wathu Mfumu Davide kuti: ‘Mulungu wanu akulitse dzina la Solomo kuposa dzina lanu ndiponso akweze ufumu wake kuposa ufumu wanu!’ Kenako mfumuyo inaweramitsa mutu wake ili pabedi.
-