1 Mafumu 1:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 Solomo anayankha kuti: “Akamachita zabwino, tsitsi lake ngakhale limodzi silidzagwera pansi, koma akadzapezeka atachita choipa,+ adzaphedwa.”
52 Solomo anayankha kuti: “Akamachita zabwino, tsitsi lake ngakhale limodzi silidzagwera pansi, koma akadzapezeka atachita choipa,+ adzaphedwa.”