4 Komanso Yehova adzakwaniritsa zimene analonjeza zokhudza ineyo zakuti: ‘Ana ako akamadzachita zinthu mosamala komanso kuyenda mokhulupirika pamaso panga ndi mtima wawo wonse ndi moyo wawo wonse,+ anthu a mʼbanja lako adzapitiriza kukhala pampando wachifumu wa Isiraeli.’+